Deuteronomo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Ukaona ng’ombe kapena nkhosa ya m’bale wako ikusochera usaisiye mwadala.+ Uziikusa ndithu ndi kuipititsa kwa m’bale wako.+
22 “Ukaona ng’ombe kapena nkhosa ya m’bale wako ikusochera usaisiye mwadala.+ Uziikusa ndithu ndi kuipititsa kwa m’bale wako.+