Levitiko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo ana a Aroni, ansembe, aziika moto paguwa lansembelo+ ndi kuyalapo nkhuni.+ Levitiko 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Aroni+ azitentha+ zinthu zimenezi paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza yomwe ili pankhuni+ zimene zili pamoto. Imeneyi ikhale nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi+ kwa Yehova. Nehemiya 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ngakhale ntchito yobweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndi mbewu zoyamba kucha. Inu Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino zimene ndinachita.+
5 Kenako ana a Aroni+ azitentha+ zinthu zimenezi paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza yomwe ili pankhuni+ zimene zili pamoto. Imeneyi ikhale nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi+ kwa Yehova.
31 ngakhale ntchito yobweretsa nkhuni+ pa nthawi zoikidwiratu ndi mbewu zoyamba kucha. Inu Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino zimene ndinachita.+