Levitiko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aziperekanso impso ziwiri+ ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta a pachiwindi,* aziwachotsa pamodzi ndi impsozo. Levitiko 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Azichotsanso impso ziwiri ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta a pachiwindi, aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.+
4 Aziperekanso impso ziwiri+ ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta a pachiwindi,* aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.
9 Azichotsanso impso ziwiri ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta a pachiwindi, aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.+