-
Levitiko 3:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Aziperekanso impso ziwiri ndi mafuta okuta impsozo, omwenso ndi mafuta a m’chiuno. Koma mafuta a pachiwindi, aziwachotsa pamodzi ndi impsozo.
-