Ekisodo 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo. Levitiko 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nyama ya nsembe yopserezayo aziisenda chikopa ndi kuidula ziwaloziwalo.+ Numeri 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno ng’ombeyo itenthedwe iyeyo akuona. Atenthe chikopa chake, nyama yake, magazi ake, limodzi ndi ndowe zake.+
14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo.
5 Ndiyeno ng’ombeyo itenthedwe iyeyo akuona. Atenthe chikopa chake, nyama yake, magazi ake, limodzi ndi ndowe zake.+