Levitiko 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kwa masiku enanso 33, mkaziyo azikhala panyumba kuti ayeretsedwe ku magazi ake. Asakhudze chilichonse chopatulika, ndipo asalowe m’malo oyera, kufikira masiku a kuyeretsedwa kwake atakwanira.+ Levitiko 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli kuti, ‘Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda ya kukha+ kumaliseche, nthenda yakeyo ndi yodetsedwa.
4 Kwa masiku enanso 33, mkaziyo azikhala panyumba kuti ayeretsedwe ku magazi ake. Asakhudze chilichonse chopatulika, ndipo asalowe m’malo oyera, kufikira masiku a kuyeretsedwa kwake atakwanira.+
2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli kuti, ‘Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda ya kukha+ kumaliseche, nthenda yakeyo ndi yodetsedwa.