Ekisodo 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ndiyeno utenge nkhosa imodzi,+ ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa nkhosayo.+ Levitiko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+
4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+