Ekisodo 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno utenge nkhosa imodzi, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa nkhosayo.+