Levitiko 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+ Levitiko 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+
3 Pamenepo azipereka mbali ina ya nsembe yachiyanjanoyo monga nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Azipereka mafuta+ okuta matumbo, mafuta onse amene ali pamatumbo.+
8 “‘Koma mafuta onse a ng’ombe ya nsembe yamachimo, aziwachotsa. Azichotsa mafuta okuta matumbo, mafuta onse okuta matumbo.+