Levitiko 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera. Numeri 26:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Koma Nadabu ndi Abihu anafa chifukwa chofukiza moto wosaloleka pamaso pa Yehova.+
9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera.