Ekisodo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa m’chihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera, kuti asapalamule mlandu ndi kufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale.+ Levitiko 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, moto unatsika kuchokera kwa Yehova ndi kuwawononga,+ moti anafa pamaso pa Yehova.+
43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa m’chihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera, kuti asapalamule mlandu ndi kufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale.+