Levitiko 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+ Numeri 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Asadziipitse pokhudza ngakhale mtembo wa bambo ake, mayi ake, m’bale wake kapena mlongo wake, iwo akamwalira.+ Asadziipitse nawo chifukwa chizindikiro cha unaziri wake kwa Mulungu chili kumutu kwake.
10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+
7 Asadziipitse pokhudza ngakhale mtembo wa bambo ake, mayi ake, m’bale wake kapena mlongo wake, iwo akamwalira.+ Asadziipitse nawo chifukwa chizindikiro cha unaziri wake kwa Mulungu chili kumutu kwake.