Ekisodo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala. Levitiko 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.
2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala.
16 Aroni ndi ana ake azidya zotsala za nsembe imeneyi.+ Azipanga mkate wopanda chofufumitsa+ ndi kudya mkatewo m’malo oyera. Aziudyera m’bwalo la chihema chokumanako.