Deuteronomo 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mwa mitundu yonse ya zinthu zokhala m’madzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chokhala ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+
9 “Mwa mitundu yonse ya zinthu zokhala m’madzi, zimene mungadye ndi izi: Chilichonse chokhala ndi zipsepse ndi mamba mungadye.+