Mateyu 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya. Luka 24:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anamupatsa chidutswa cha nsomba yowotcha,+
18 Pamene anali kuyenda m’mbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba m’nyanja, pakuti anali asodzi. Mayina awo anali Simoni+ wotchedwa Petulo+ ndi Andireya.