Yobu 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ana ake amakhalira kumwa magazi.Kumene kuli zakufa, icho chimakhala komweko.”+ Mateyu 24:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kulikonseko kumene kuli thupi lakufa, ziwombankhanga+ zimasonkhana komweko.+