-
Levitiko 14:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Pamenepo wansembe amene wagamula kuti munthuyo ndi woyera, azikaonetsa amene akudziyeretsayo, ndi zinthu zakezo kwa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako.
-