Levitiko 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Muzisunga masabata anga+ ndipo muziopa malo anga opatulika.+ Ine ndine Yehova. Numeri 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+ Numeri 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, ameneyo aphedwe+ kuti asakhalenso pakati pa mpingowo, chifukwa waipitsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera. Choncho ndi wodetsedwa.
3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+
20 “‘Koma munthu wodetsedwa akapanda kudziyeretsa, ameneyo aphedwe+ kuti asakhalenso pakati pa mpingowo, chifukwa waipitsa malo opatulika a Yehova. Iye sanawazidwe madzi oyeretsera. Choncho ndi wodetsedwa.