Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho uzipereka ng’ombe ya nsembe yamachimo tsiku ndi tsiku kuti iphimbe machimo.+ Pamenepo uziyeretsa guwa lansembe ku machimo mwa kuliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza+ kuti likhale loyera.

  • Levitiko 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Mose anapha+ ng’ombeyo, ndipo anatenga magazi+ ake ndi kuwapaka ndi chala chake panyanga zonse za guwa lansembe, n’kuyeretsa guwalo ku uchimo. Koma magazi otsalawo anawathira pansi pa guwa lansembe kuti alipatule, kuphimba machimo+ paguwalo.

  • Levitiko 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Akatero azituluka ndi kupita kuguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova kuti akaliphimbire machimo. Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongo ndi a mbuzi n’kuwapaka panyanga zonse za guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena