Levitiko 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Akatero azisamba thupi lonse+ m’malo oyera+ ndi kuvala zovala zake.+ Kenako azituluka kukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+ 1 Yohane 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ndi nsembe+ yophimba+ machimo athu.+ Osati athu+ okha, komanso a dziko lonse lapansi.+
24 Akatero azisamba thupi lonse+ m’malo oyera+ ndi kuvala zovala zake.+ Kenako azituluka kukapereka nsembe yake yopsereza+ ndi nsembe yopsereza ya anthuwo+ ndipo aziphimba machimo ake ndi a anthuwo.+