Levitiko 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense wa inu akadzachita chilichonse mwa zinthu zonse zonyansazi, anthu ochita zimenezi adzaphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.+ Levitiko 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli, ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli, wopereka mwana wake aliyense kwa Moleki,*+ aziphedwa ndithu. Nzika za m’dziko lanu zizimupha mwa kum’ponya miyala.
29 Aliyense wa inu akadzachita chilichonse mwa zinthu zonse zonyansazi, anthu ochita zimenezi adzaphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana a Isiraeli, ndiponso mlendo aliyense wokhala mu Isiraeli, wopereka mwana wake aliyense kwa Moleki,*+ aziphedwa ndithu. Nzika za m’dziko lanu zizimupha mwa kum’ponya miyala.