Ekisodo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+ Deuteronomo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+
31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+
21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+