Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 30:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo, Leya anayankha Rakele kuti: “Kodi ukuyesa ndi nkhani yaing’ono kuti iweyo unatenga mwamuna wanga?+ Tsopano ukufuna kutenganso mandereki a mwana wanga?” Ndipo Rakele anati: “Pa chifukwa chimenechi, usiku walero mwamunayu agona ndi iwe kuti tisinthane ndi mandereki a mwana wakowa.”

  • 1 Samueli 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mkazi mnzake wa Hana anali kum’sautsa+ kwambiri n’cholinga choti amukhumudwitse, chifukwa chakuti Yehova anali atatseka mimba yake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena