15 Pamenepo, Leya anayankha Rakele kuti: “Kodi si zokwanira kuti unatenga mwamuna wanga?+ Ndiye pano ukufuna kutenganso mandereki a mwana wanga?” Choncho Rakele anati: “Chabwino, usiku walero mwamunayu agona ndi iwe kuti tisinthane ndi mandereki a mwana wakowa.”