Ekisodo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kenako upereke ng’ombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ng’ombeyo.+ Levitiko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+
10 “Kenako upereke ng’ombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ng’ombeyo.+
4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+