Ekisodo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako ubweretse ngʼombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ngʼombeyo.+
10 Kenako ubweretse ngʼombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ngʼombeyo.+