Miyambo 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amene amabera mwachinyengo munthu wonyozeka kuti apeze zinthu zambiri,+ komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera, ndithu adzasauka.+ Maliko 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+
16 Amene amabera mwachinyengo munthu wonyozeka kuti apeze zinthu zambiri,+ komanso wopereka mphatso kwa munthu wolemera, ndithu adzasauka.+
19 Iwe umadziwa malamulo akuti, ‘Usaphe munthu,*+ Usachite chigololo,+ Usabe,+ Usapereke umboni wonama,+ Usachite chinyengo+ ndiponso lakuti Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’”+