Ekisodo 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+ Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+
29 “Zovala zopatulika+ za Aroni zidzakhala za ana ake+ obwera m’mbuyo mwake. Adzawadzoza+ ndi kuwapatsa mphamvu atavala zovala zimenezi.+