Levitiko 11:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 kuti muzisiyanitsa+ chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simuyenera kudya.’” Deuteronomo 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya nyama zimene muyenera kudya ndi izi:+ ng’ombe, nkhosa, mbuzi, Machitidwe 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anati: “Iyayi Ambuye, sindinadyepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chikhalire.”+
47 kuti muzisiyanitsa+ chodetsedwa ndi choyera komanso zamoyo zimene muyenera kudya ndi zimene simuyenera kudya.’”
14 Koma Petulo anati: “Iyayi Ambuye, sindinadyepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chikhalire.”+