Levitiko 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 kuti muzisiyanitsa pakati pa chinthu chopatulika ndi choipitsidwa ndiponso pakati pa chodetsedwa ndi choyera.+ Levitiko 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse+ ndi nyama, mbalame kapena chilichonse choyenda padziko lapansi, chimene ine ndachipatula kuti musadye pogamula kuti ndi chodetsedwa. Ezekieli 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+ Ezekieli 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu choipitsidwa. Aziwaphunzitsa kuti adziwe kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi choyera.+
10 kuti muzisiyanitsa pakati pa chinthu chopatulika ndi choipitsidwa ndiponso pakati pa chodetsedwa ndi choyera.+
25 Muzisiyanitsa nyama yoyera ndi yodetsedwa, mbalame yodetsedwa ndi yoyera.+ Musadziipitse+ ndi nyama, mbalame kapena chilichonse choyenda padziko lapansi, chimene ine ndachipatula kuti musadye pogamula kuti ndi chodetsedwa.
26 Ansembe ako aphwanya chilamulo changa modzionetsera,+ ndipo akuipitsa malo anga oyera.+ Sakusiyanitsa+ zinthu zoyera ndi zinthu wamba.+ Sanauze anthu kusiyana kwa zinthu zodetsedwa ndi zinthu zoyera.+ Anyalanyaza sabata langa+ ndipo andichitira mwano pakati pawo.+
23 “‘Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu choipitsidwa. Aziwaphunzitsa kuti adziwe kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi choyera.+