Ezekieli 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+ Aroma 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.
20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+
24 Pakuti “dzina la Mulungu likunyozedwa pakati pa anthu amitundu chifukwa cha inu”+ monga mmene Malemba amanenera.