Ezekieli 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “‘Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu choipitsidwa. Aziwaphunzitsa kuti adziwe kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi choyera.+
23 “‘Iwo aziphunzitsa anthu anga za kusiyana kwa chinthu chopatulika ndi chinthu choipitsidwa. Aziwaphunzitsa kuti adziwe kusiyana kwa chinthu chodetsedwa ndi choyera.+