Numeri 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+ Aheberi 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo m’malo oyera chifukwa cha machimo, amakazitentha kunja kwa msasa.+
3 Kaya akhale mwamuna kapena mkazi, uziwatulutsa kunja kwa msasa+ kuti asadetse+ misasa ya anthu amene ine ndikukhala pakati pawo.”+
11 Pakuti nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo m’malo oyera chifukwa cha machimo, amakazitentha kunja kwa msasa.+