Levitiko 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo wansembe azitentha+ zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya,+ kuti chikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova. Numeri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.
11 Ndipo wansembe azitentha+ zinthu zonsezi paguwa lansembe monga chakudya,+ kuti chikhale nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.
5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.