Ekisodo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa m’chihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera, kuti asapalamule mlandu ndi kufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale.+ Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.
43 Aroni ndi ana ake azivala makabudula amenewa polowa m’chihema chokumanako kapena popita kuguwa lansembe kukatumikira pamalo oyera, kuti asapalamule mlandu ndi kufa. Limeneli ndi lamulo kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale.+
3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.