Ekisodo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Guwalo uliike kutsogolo kwa nsalu yotchinga imene ili pafupi ndi likasa la umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni,* pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+ Aheberi 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+
6 Guwalo uliike kutsogolo kwa nsalu yotchinga imene ili pafupi ndi likasa la umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni,* pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+
20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+