Levitiko 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+ Salimo 83:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+ Salimo 135:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo mpaka kalekale.+Inu Yehova, dzina lanu* lidzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+
18 Kuti anthu adziwe+ kuti inu, amene dzina lanu ndinu Yehova,+Inu nokha ndinu Wam’mwambamwamba,+ wolamulira dziko lonse lapansi.+
13 Inu Yehova, dzina lanu lidzakhalapo mpaka kalekale.+Inu Yehova, dzina lanu* lidzakhalapo ku mibadwomibadwo.+