Ekisodo 29:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzayeretsa chihema chokumanako ndi guwa lansembe. Ndidzayeretsanso+ Aroni ndi ana ake kuti atumikire monga ansembe anga. Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete. Ezara 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako ndinawauza kuti: “Inu ndinu oyera+ kwa Yehova. Ziwiyazi+ ndi zopatulika ndipo siliva ndi golideyu ndi nsembe yaufulu yopita kwa Yehova Mulungu wa makolo anu.
44 Ndidzayeretsa chihema chokumanako ndi guwa lansembe. Ndidzayeretsanso+ Aroni ndi ana ake kuti atumikire monga ansembe anga.
3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.
28 Kenako ndinawauza kuti: “Inu ndinu oyera+ kwa Yehova. Ziwiyazi+ ndi zopatulika ndipo siliva ndi golideyu ndi nsembe yaufulu yopita kwa Yehova Mulungu wa makolo anu.