Levitiko 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Asaipitse ana ake pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndam’patula.’”+ Levitiko 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera. Yohane 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+
9 “‘Chotero azisunga malamulo anga kuti asasenze tchimo ndi kufa,+ chifukwa chosasunga malamulowo ndi kuipitsa zinthu zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndawapatula monga anthu oyera.
36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+