Levitiko 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni, kuti, ‘Aliyense wa inu asadziipitse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.*+ Numeri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aliyense wokhudza mtembo wa munthu aliyense,+ nayenso azikhala wodetsedwa masiku 7.+ Numeri 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chilichonse chimene munthu wodetsedwayo angakhudze, chikhale chodetsedwa.+ Komanso munthu amene angakhudze chinthucho, akhale wodetsedwa mpaka madzulo.’”+
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni, kuti, ‘Aliyense wa inu asadziipitse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.*+
22 Chinthu chilichonse chimene munthu wodetsedwayo angakhudze, chikhale chodetsedwa.+ Komanso munthu amene angakhudze chinthucho, akhale wodetsedwa mpaka madzulo.’”+