21Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni, kuti, ‘Aliyense wa inu asadziipitse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.*+
9 Koma ngati munthu wina wafera pambali pake mwadzidzidzi,+ moti Mnaziriyo waipitsa mutu umene uli ndi chizindikiro cha unaziri wake pokhudza mtembowo, amete tsitsi+ la kumutu kwake pa tsiku la kuyeretsedwa kwake. Alimete pa tsiku la 7.
6 Tsopano panali amuna ena amene anadzidetsa pokhudza mtembo wa munthu,+ moti sanathe kukonza nsembe ya pasika pa tsikulo. Chotero anakaonekera kwa Mose ndi Aroni pa tsikulo.+