Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye asayandikire munthu wakufa+ ndipo asadziipitse bambo ndi mayi ake akamwalira.

  • Numeri 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche,+ ndi aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza mtembo wa munthu.+

  • Numeri 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Masiku onse amene iye ali wodzipereka kwa Yehova, asamakhudze mtembo.+

  • Numeri 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Ngati munthu angafere muhema, nali lamulo lake: Munthu aliyense wolowa muhemamo, ndi aliyense amene ali mmenemo, akhale wodetsedwa masiku 7.

  • Numeri 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Aliyense amene wakhudza mtembo wa munthu amene waphedwa ndi lupanga,+ kapena mtembo uliwonse, kapenanso fupa la munthu,+ ngakhalenso manda a munthu, akhale wodetsedwa masiku 7.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena