Numeri 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano panali amuna ena amene anadzidetsa chifukwa chokhudza mtembo wamunthu,+ moti sanathe kukonza nsembe ya Pasika pa tsikulo. Choncho amunawo anakaonekera kwa Mose ndi Aroni pa tsikulo,+
6 Tsopano panali amuna ena amene anadzidetsa chifukwa chokhudza mtembo wamunthu,+ moti sanathe kukonza nsembe ya Pasika pa tsikulo. Choncho amunawo anakaonekera kwa Mose ndi Aroni pa tsikulo,+