Numeri 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Ngati mlendo wokhala pakati panu, kapena mlendo amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, afunikira kupereka nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova, monga mmene inuyo muzichitira, iyenso azichita momwemo.+ Numeri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakhale malamulo ndi zigamulo zofanana kwa inu ndi kwa alendo amene akukhala nanu.’”+
14 “‘Ngati mlendo wokhala pakati panu, kapena mlendo amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, afunikira kupereka nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova, monga mmene inuyo muzichitira, iyenso azichita momwemo.+