Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “M’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muzidzisautsa*+ ndipo aliyense wa inu asamagwire ntchito ina iliyonse,+ kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu. Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale.+

  • Levitiko 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Munthu aliyense amene wadya nyama imene waipeza yakufa, kapena yophedwa ndi chilombo,+ kaya akhale nzika kapena mlendo wokhala pakati panu, munthu ameneyo azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa kufikira madzulo.+ Kenako azikhala woyera.

  • Numeri 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Ngati mlendo wokhala pakati panu, kapena mlendo amene wakhala nanu kwa mibadwomibadwo, afunikira kupereka nsembe yotentha ndi moto yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova, monga mmene inuyo muzichitira, iyenso azichita momwemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena