15 Ngati munthu aliyense wadya nyama imene waipeza yakufa kapena imene yaphedwa ndi chilombo,+ kaya akhale nzika kapena mlendo wokhala pakati panu, munthu ameneyo azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Kenako azikhala woyera.