Levitiko 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Tsiku la 10 m’mwezi wa 7 umenewu ndi tsiku la mwambo wophimba machimo.+ Muzichita msonkhano wopatulika ndipo muzidzisautsa*+ ndi kupereka nsembe+ yotentha ndi moto kwa Yehova. Numeri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+
27 “Tsiku la 10 m’mwezi wa 7 umenewu ndi tsiku la mwambo wophimba machimo.+ Muzichita msonkhano wopatulika ndipo muzidzisautsa*+ ndi kupereka nsembe+ yotentha ndi moto kwa Yehova.
7 “‘Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzidzisautsa.*+ Musamagwire ntchito yamtundu uliwonse.+