Numeri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu.* Musamagwire ntchito iliyonse.+
7 Pa tsiku la 10 la mwezi wa 7 umenewu, muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzisonyeza kuti mukudzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu.* Musamagwire ntchito iliyonse.+