29 “M’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muzidzisautsa*+ ndipo aliyense wa inu asamagwire ntchito ina iliyonse,+ kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu. Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale.+
27 “Tsiku la 10 m’mwezi wa 7 umenewu ndi tsiku la mwambo wophimba machimo.+ Muzichita msonkhano wopatulika ndipo muzidzisautsa*+ ndi kupereka nsembe+ yotentha ndi moto kwa Yehova.