Levitiko 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamagwire ntchito iliyonse.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.
31 Musamagwire ntchito iliyonse.+ Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.